1
Mlaliki 10:10
Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
CCL
Ngati nkhwangwa ili yobuntha yosanoledwa, pamafunika mphamvu zambiri potema, koma luso limabweretsa chipambano.
Compare
Explore Mlaliki 10:10
2
Mlaliki 10:4
Ngati wolamulira akukwiyira, usachoke pa ntchito yako; kufatsa kumakonza zolakwa zazikulu.
Explore Mlaliki 10:4
3
Mlaliki 10:1
Monga ntchentche zakufa zimayika fungo loyipa mʼmafuta onunkhira, choncho kupusa pangʼono kumawononganso nzeru ndi ulemu.
Explore Mlaliki 10:1
4
Mlaliki 10:12
Mawu a pakamwa pa munthu wanzeru ndi okondweretsa, koma chitsiru chidzawonongedwa ndi milomo yake yomwe.
Explore Mlaliki 10:12
5
Mlaliki 10:8
Amene amakumba dzenje adzagwamo yekha; amene amabowola khoma adzalumidwa ndi njoka.
Explore Mlaliki 10:8