1
Mal. 4:5-6
Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa
BLY-DC
“Koma lisanafike tsiku lalikulu loopsalo la Chauta, ndidzakutumizirani mneneri Eliya. Iyeyo adzayanjanitsa atate ndi ana ao, ana ndi atate ao, kuwopa kuti ndingadzabwere kudzatemberera dziko lanu kuti liwonongeke.”
مقایسه
Mal. 4:5-6 را جستجو کنید
2
Mal. 4:1
Chauta Wamphamvuzonse akunena kuti, “Tsiku likubwera pamene anthu onse odzikuza ndi ochita zoipa adzapsa ngati chiputu m'ng'anjo. Tsiku limenelo adzapserereratu osatsalako muzu kapena nthambi. Ndikutero Ine Chauta Wamphamvuzonse.
Mal. 4:1 را جستجو کنید