لوگو یوورژن
كتاب‌ مقدسبرنامه‌های مطالعهویدیوها
دانلود برنامه
انتخاب زبان
ایکن جستجو

آیات محبوب کتاب مقدس از MACHITIDWE 9

1

MACHITIDWE 9:15

Buku Lopatulika

BLP-2018

Koma Ambuye anati kwa iye, Pita; pakuti iye ndiye chotengera changa chosankhika, chakunyamula dzina langa pamaso pa amitundu ndi mafumu ndi ana a Israele

مقایسه

MACHITIDWE 9:15 را جستجو کنید

2

MACHITIDWE 9:4-5

Buku Lopatulika

BLP-2018

ndipo anagwa pansi, namva mau akunena naye, Saulo, Saulo, Undilondalonderanji? Koma anati, Ndinu yani Mbuye? Ndipo anati, Ndine Yesu amene umlondalonda

مقایسه

MACHITIDWE 9:4-5 را جستجو کنید

3

MACHITIDWE 9:17-18

Buku Lopatulika

BLP-2018

Ndipo anachoka Ananiya, nalowa m'nyumbayo; ndipo anaika manja ake pa iye, nati, Saulo, mbale, Ambuye wandituma ine, ndiye Yesu amene anakuonekerani panjira wadzerayo, kuti upenyenso, ndi kudzazidwa ndi Mzimu Woyera. Ndipo pomwepo padagwa kuchoka m'maso mwake ngati mamba, ndipo anapenyanso; ndipo ananyamuka nabatizidwa

مقایسه

MACHITIDWE 9:17-18 را جستجو کنید

برنامه های خواندنی رایگان و عبادات مربوط به MACHITIDWE 9

باب‌ قبلی
باب بعدی
یوورژن

به چالش کشیدن و تشویق هر روزه شما برای ایجاد رابطه صمیمی تر با خدا .

خدمت

دربارهٔ

مشاغل

داوطلب شوید.

بلاگ

مطبوعات

لینک‌های مفید

پشتیبانی

اهدای کمک مالی

ترجمه‌های کتاب‌مقدس

کتاب‌ مقدس صوتی

ترجمه‌های موجود کتاب‌مقس

آیۀ روز


یک خدمت دیجیتالی از

لایف‌چرچ
فارسی

©2026 لایف چرچ / یوورژن

قوانین حفظ حریم شخصیشرايط
برنامه افشای آسیب پذیری
فیس‌بوکتویتراینستاگرامبرنامه یوتیوببرنامه پین ترست