1
MACHITIDWE 3:19
Buku Lopatulika
BLP-2018
Chifukwa chake lapani, bwererani kuti afafanizidwe machimo anu, kotero kuti zidze nyengo zakutsitsimutsa zochokera kunkhope ya Ambuye
مقایسه
MACHITIDWE 3:19 را جستجو کنید
2
MACHITIDWE 3:6
Koma Petro anati, Siliva ndi golide ndilibe; koma chimene ndili nacho, ichi ndikupatsa, M'dzina la Yesu Khristu Mnazarayo, yenda.
MACHITIDWE 3:6 را جستجو کنید
3
MACHITIDWE 3:7-8
Ndipo anamgwira iye kudzanja lake lamanja, namnyamutsa; ndipo pomwepo mapazi ake ndi mfundo za kumapazi zinalimbikitsidwa. Ndipo anazunzuka, naimirira, nayenda; ndipo analowa pamodzi nao mu Kachisi, nayenda, nalumpha, nayamika Mulungu.
MACHITIDWE 3:7-8 را جستجو کنید
4
MACHITIDWE 3:16
Ndipo pa chikhulupiriro cha m'dzina lake dzina lakelo linalimbikitsa iye amene mumuona, nimumdziwa; ndipo chikhulupiriro chili mwa Iye chinampatsa kuchira konse kumeneku pamaso pa inu nonse.
MACHITIDWE 3:16 را جستجو کنید