1
MACHITIDWE 22:16
Buku Lopatulika
BLP-2018
Ndipo tsopano uchedweranji? Tauka, nubatizidwe ndi kusamba kuchotsa machimo ako, nuitane pa dzina lake.
مقایسه
MACHITIDWE 22:16 را جستجو کنید
2
MACHITIDWE 22:14
Ndipo anati, Mulungu wa makolo athu anakusankhiratu udziwe chifuniro chake, nuone Wolungamayo, numve mau otuluka m'kamwa mwake.
MACHITIDWE 22:14 را جستجو کنید
3
MACHITIDWE 22:15
Ndipo udzamkhalira Iye mboni kwa anthu onse, za izo udaziona ndi kuzimva.
MACHITIDWE 22:15 را جستجو کنید