1
MACHITIDWE 19:6
Buku Lopatulika
BLP-2018
Ndipo pamene Paulo anaika manja ake pa iwo, Mzimu Woyera anadza pa iwo; ndipo analankhula ndi malilime, nanenera.
مقایسه
MACHITIDWE 19:6 را جستجو کنید
2
MACHITIDWE 19:11-12
Ndipo Mulungu anachita zamphamvu za pazokha ndi manja a Paulo; kotero kuti anamuka nazo kwa odwala nsalu zopukutira ndi za pantchito, zochokera pathupi pake, ndipo nthenda zinawachokera, ndi ziwanda zinatuluka.
MACHITIDWE 19:11-12 را جستجو کنید
3
MACHITIDWE 19:15
Ndipo unayankha mzimu woipa, nuti kwa iwo, Yesu ndimzindikira, ndi Paulo ndimdziwa, koma inu ndinu ayani?
MACHITIDWE 19:15 را جستجو کنید