Alom 15
15
Athangatileni wina
1Ife yao takwima mchikhulupi ifunuka taathangatile anyiwajha afooka, kuti ayakhoze mavuto yao. Tisidajhikondelela tachinawene pe. 2Tifunika kwa thangatila wina pakuchita vabwino, ni kwachita aime kwa Ambuye. 3Pakuti Kilisito siwadachite vindhu va kujhikondwelecha mwene, nambho wadali ngati umo yalembedwela mlembo, “Matukwano yawo yajha adakutukwana iwe yadanipata ine uyo udanisanghula,” 4Pakuti yonjhe yayo yadalembedwa mmalembo ya Mnungu, yadalembedwa ndande ya kutiyaluza ife, malembo yameneyo yatithangatila kulimba mtima mumavuto yathu ni kutitondeza, tikhoze kukhala ni chikhulupi. 5Mnungu nde uyo watithila mtima ni nde uyo watichita tilimbe mtima. Chipano nipembha kuti, wachitichite mukhale kwa maganizo yamojhi, ndande mwachata Ambuye Yesu. 6Kuti anyiimwe kwapamojhi ni mvekelo umojhi, mumtamande Mnungu Tate wa Ambuye wathu Yesu Kilisito.
Uthenga Wabwino kwa wandhu wonjhe
7Chipano landilanani anyiimwe kwa anyiimwe ndande ya ulemelelo wa Mnungu ngati kilisito umo wadakulandilani anyiimwe kuti wandhu amtamande Mnungu. 8Pakuti nikukambilani Kilisito wadatumikila Ayahudi wapate kulangiza kukhulupilika kwa Mnungu, ni yajha wadakamba Mnungu kuti siwapache azee watu yakhoze kukwana. 9Chimchijha kuti nawo wandhu amaiko yina akhoze kumtamnda Mnungu ndande ya lisungu lake. Ngati umo yalembedwa mmalembo ya Mnungu,
“Chipano sinikutamande pakati pa wandhu amaiko yina.
Siniimbe matamando ya jhina lanu.”
10Malembo yakamba chimwechi,
“Kondwelani anyiimwe wandhu amaiko yina,
kondwelani pamojhi ni wandhu wa Ambuye.”
11Ni chipano,
“Anyiimwe wandhu amaiko yonjhe, atamandeni Ambuye,
anyiimwe wandhu wonjhe mtamandeni Ambuye.”
12Isaya wadakamba,
“Siwachokele mwana kukhamu la Yese,
niiye siwachogoze wandhu amaiko yonjhe,
nianyiiwo samkhulupilile kuti iye siwaombole.”
13Mnungu wa chikhulupi uyo wakuthilani anyiimwe mtima ni mtendele pa kumkhulupilila, mpate kujhazidwa ni chikhululupilo chachikulu kwa mbhavu za mzimu wa Mnungu.
Dala la Poolo kulemba chikalalakala ichi
14Achabale wanga ine nane nijhiwa kuti anyiimwe mwajhala ubwino, elimu, ni mkhoza kuyaluzana anyiimwe kwa anyiimwe. 15Nambho nakulembelani vindhu vambili mkalata iyi popande mandha, nikhoze kukumbuchani nghani ya vindhu vakuti. Nachita chimwecho ndande ya ubwino uwo wanipacha Mnungu, 16ubwino wa ine kukhala mtumiki wa Yesu Kilisito kwa wandhu a maiko yina. Ni njhito yanga ya chijhukulu, kuuzila Uthenga Wabwino wa Mnungu dala wandhu amaiko yina akhoze kukhala njhembe yopyeleza iyo ivomelezeka ni Mnungu, njhembe iyo yaelechedwa ni Mzimu wa Mnungu. 17Chipano ngati nalunjana ni Kilisito Yesu, nikhoza kujhidamila njhito yanga ndande ya Mnungu. 18Siniyesa kukamba chindhu china chalichonjhe, nambho chijhape Yesu Kilisito wachichita kwa kunitumia ine dala wandhu amaiko yina akhoze kumvela Mnungu. Wachita chimwecho kwa mawu ni vichito, 19kwa mbhavu zochita vodabwicha ni vozizwicha, ni kwa mbhavu za Mzimu wa Mnungu. Basi kwa kumanga ulendo malo yonjhe, kuyambila kujha ku Yelusalemu mbaka ku Iluliko, naulalikila mokwanila Uthenga Wabwino wa Kilisito. 20Ichonifuna ni kulalikila Uthenga Wabwino pamalo paliponjhe yapo jhina la Kililsto lidavekele, nisinidajha kuyambicha njhito pamalo yapo mundhu mwina watoyambicha. 21Ngati umo yalembedwela mmalembo ya Mnungu,
“Wandhu wonjhe yao sadakambidwe nghani zake saone,
anyiwajha sadavele sajhiwe.”
Poolo waganizila kupita kumujhi wa Loma
22Njhito imeneyo yanichita nikhale ni vindhu vambili, ni mala zambili nidachekelezedwa kujha kukuonani. 23Nambho saino ndande namaliza njhito yanga malo yano, ni pakuti vyaka vambili nimakumbila kujha kwanu, 24nikhumbila kupunda kujha kwanu ni yapo sinikhale mnjila kupita ku Hisipania. Nikhumbila kukuonani pa ulendo wanga, ni anyiimwe mnimangiche ulendo wopita kumeneko, pambuyo pa kukondwela kukhala pamojhi ni anyiimwe. 25Nambo kwachipano nipita kuchita njhito ya Mnungu, ndande ya wandhu aku Yelusalemu. 26Pakuti wandhu amkhulupilila Yesu ku Makedoniya ni Akaya alamula kuchocha vindhu vyao ndande ya kwathangatila wandhu a Mnungu yao aliosauka Yelusalemu. 27Anyiiwo alamula kuchita chimwecho, nambho kwa uzene imeneyo ni njhito yao ku Yelusalemu. Pakuti wandhu a maiko yina apata mwawi wa Chizimu wa Ayahudi, nyiawiiwo afunika atangatile Ayahudi ivo avifuna pano pajhiko. 28Yapo sinikwaniliche njhito imeneyo ni kwapaacha vindhu vidakusidwa ndande yao, sinikuendeleni anyiimwe yapo sinikhale muulendo wopita ku Hisipania. 29Nijhiwa kuti nikajha kwanu, Kilisito siwakupacheni mwawi kupanda.
30Chipano anyabale wanga, nikupembhelani kwa ambuye Yesu Kilisito ni kwa chikondi icho chipelekedwa ni Mzimu wa Mnungu, mkhale pamojhi niine pa kunipembhela kwa Mnungu. 31Mnipembhele kuti sinidapwetekedwa mmanja mwa wajha sadakhulupilile wayo ali ku Yudea, ni utumiki wanga ukhoze kuvomelezedwa ni wandhu Amnungu yao ali ku Yelusalemu. 32Chimwecho, Mnungu wakakonda sinikhoze kujha kwanu, ni mtima wa wakukondwela, nipumulile pamojhi ni anyiimwe. 33Mnungu uyo wapeleka mtendele wakhale pamojhi ni anyiimwe mwawonjhe! Ikhale chimwecho!
Currently Selected:
Alom 15: NTNYBL2025
Highlight
Share
Copy
Want to have your highlights saved across all your devices? Sign up or sign in
The New Testament in Nyanja @The Word for The World International and Nyanja Language translation, 2025. All rights reserved.

: