Maluko 8:37-38
Maluko 8:37-38 NTNYBL2025
Mundhu siwachoche chiyani kuti wakhoze kuombola umoyo wake? Mundhu waliyonjhe uyo wanionela njhoni ine ni Uthenga Wabwino pa mbadwa wachipano uwo wakana kumjhiwa Mnungu ni kuchita voipa, ine Mwana wa Mundhu nane sinimkane mundhu mmeneyo, yapo sinijhe pa ulemelelo wa Atate wanga ni wa atumiki oyela akumwamba.”