YouVersion Logo
Search Icon

Yohana 19

19
1Ndiipo, Pilato wadaalamula amtenge Yesu wabulidwe mikwapulo. 2Chimwecho asikali adakonja nghata ya minga, adamveka kumutu, adamveka ni njhalu ya itali ya chifumu ya zambalau. 3Amakwela tetete ni kujha yapo wali Yesu mujha mnyumba ya chifumu niakamba, “Moni, Mfumu wa Ayahudi!” Uku niadaendekela kumbula vimbhama kumaso.
4Pilato wadatulukanjho kubwalo, wadaakambila, “Mjhiwe kuti ine sinidaone cholakwa chililonjhe kwake, chipano nimpeleka kwanu.” 5Chimwecho Yesu wadatuluka kubwalo wavala chisoti cha minga ni njhalu ya itali ya chifumu ya zambalau. Pilato wadamkambila, “Mundhu wanu yuno pano.”
6Ajhukulu waakulu ni alonda anyumba ya Amnungu yapo adamuona adakweza mvekelo, “Mpachikeni! Mpachikeni!”
Ndiipo Pilato wadaakambila, “Mtengeni mwachinawene, mkampachike ndande ine sinidaone cholakwa chilichonjhe cha kumlamula.”
7Ndiipo Ayahudi adamuyangha, “Ife tilinalo thauko, ni kwa thauko limenelo, wafunika wamwalile, ndande iye wamajhichita kuti ni Mwana wa Amnungu.”
8Yapo wadaendekela kuvela mawu yameneyo, Pilato wadaopa kupunda. 9Chimwecho, wadamtenga Yesu ni kulowanayo mkati mwa nyumba ya chifumu, wadamfunjha Yesu, “Wachokela kuti iwe?”
Nambho Yesu siwadamuyanghe kandhu. 10Chimwecho Pilato wadamkambila, “Siukamba nane? Siujhiwa kuti nili ni lamulo la kukumasula ni lamulo lakukupachika pamtanda?”
11Yesu wadamuyangha, “Siudakakhala ni lamulo lalilonjhe kwanga ngati siudaka pachidwa ni Amnungu. Ndande imeneyo uyo waniika mmanja mwako wali ni machimo yayakulu kupunda.”
12Kuyambila pamenepo Pilato wamafuna njila ya kumsiilila, nambho Ayahudi adakweza mvekelo adakamba, “Ukamsiilila uyu, iwe asati bwenji lake Kaisali, waliyonjhe uyo wajhichita mfumu wamchucha Kaisali!”
13Ndiipo Pilato yapo waadavela mawu yameneyo wadamtulucha Yesu kubwalo, wadakhala pampando wa ulamuli pamalo yapo patanidwa “Gabata” Mate yake sakafu ya Myala.
14Idali ngati sasita za usana, siku yokonjekela Pasaka. Pilato wadaakambila Ayahudi, “Mfumu wanu yuno pano!”
15Adakweza mvekelo, “Mchoche! Mchoche!”
Pilato wadafunjha, “Nimpachike pamtanda Mfumu wanu?”
Ajhukulu waakulu adayangha, “Ife tilibe Mfumu mwina nambho Kaisali pe!”
16Chimwecho, Pilato wadaapacha Yesu kuti ampachike achinawene.
Yesu wapachikidwa pamtanda
Matayo 27:32-44; Maluko 15:21-32; Luka 23:26-43
Ndiipo, adamtenga Yesu. 17Yesu wadautenga mtanda wake, wadachokapo ni kupita pamalo yapo pamatanidwa kwa Chihebulaniya, “Gholighota” Mate yake fuvu la mutu. 18Pamenepo nde yapo adammpachika pamtanda, wandhu wina awili adapachikidwa pamojhi ni iye, mmojhi wadapachikidwa pamtanda wake udali jhanja la kwene mwina pamtanda wake udali jhanja la kumanjele, Yesu wadali pakati pao. 19Pilato wadalemba pa chibao, “Yesu wa ku Nazaleti, Mfumu wa Ayahudi,” ni kuika pamwamba pamtanda wa Yesu. 20Wandhu ambili adasoma nghani imeneyo, pakuti pamalo yapo Yesu adampachika padali pafupi ni mujhi. Nghani imeneyo idalembedwa kwa Chihebulania, Kilatini ni chigiliki. 21Ndipo ajhukulu wakulu akulu adamkambila Pilato, “Siudalemba, ‘Mfumu wa Ayahudi,’ nambho lemba, ‘Mundhu uyu wamakamba kuti, Ine Mfumu wa Ayahudi.’ ”
22Pilato wadayangha, “Yayo nalemba, nalemba!”
23Asikali adampachika Yesu, adazitenga njhalu zake, adazighawa malundo yanai, kila asikali lundo limojhi. Adatenga njhalu yake yaitali iyo idasokedwa chipande chimojhi, popande msoko. 24Asikali adakambilana, “Njhalui tisadaing'amba, nambho tibule kula siikhale ya yani.” Chindhu ichi chidachitika dala yakwanile malembo yo yela yakamba,
“Adaghawana vivalo vanga,
Njhalu yanga aibulila kula.”
Chimwecho nde umo adachitila asikali ameneo.
25Pafupi ni mtanda wa Yesu adaima amaye wake, akulu wao wa amake, Malia wamkazi wa Kileopa, ni Malia uyo wadachokela kumujhi wa Magidala. 26Yesu yapo wadaona amake aima pafupi ni oyaluzidwa uyo wamamkonda, wadaakambila amaye wake, “Maye! Mwana wanu uyo yapo.”
27Ndiipo wadamkambila yujha oyaluzidwa wake Yohana, “Amaye wako yawo yapo.” Kuyambila ndhawi imeneyo oyaluzidwayo wadatengedwa ni amaye wake Ayesu kukhala kukhomo kwao.
Yesu wamwalila
Matayo 27:45-56; Maluko 15:33-41; Luka 23:44-49
28Chimwecho Yesu yapo wadajhiwa yonjhe yakwanila, dala Malembo yakwanile, wadakamba, “Niona lujho.”
29Pamwepo lidalipo bakuli yajhala divai. Ndiipo, adabiza buula mudivai adanyeka mumtengo wa hisopo, ni kumuika mkamwa wafifinye. 30Yesu yapo wadanyambita divai imeneyo, wadakamba, “Njhito yatha!” ndiipo wadakwatamicha mutu, ni kumwalila.
Asikali amlasa Yesu msongha mundhiti
31Idali ijhuma, siku lo jhikonjekela. Dala matupi siyadakhala pamtanda Siku lo Pumulila, ndande siku lo Pumulila limenelo lidagwela pa nyengo ya pwando la Pasaka, Ayahudi adampembha Pilato myendo ya wajha adapachikidwa ityoledwe ni matupi yao yachochedwe pamitanda. 32Ndipo, mlonda wadapita kuithyola myendo yayujha mundhu oyamba ni yujha wakawili yawo adapachikidwa pamojhi ni Yesu. 33Yapo adafika kwa Yesu, adaona kuti wamwalila, chimwecho sadathyole myendo. 34Chimwecho mmojhi wa asikali wadamlasa msonga mndhiti, pamwepo udachoka mwazi ni majhi. 35Mundhu uyo wadaona vindhu vimenevo nde uyo wadachocha umboni, umboni wake wa zene. Ni yayo wakamba yazene, nayo wachocha umboni dala mkhoze kukhulupilila. 36Yameneyo yadachokela dala yakwanile Malembo Yoyela, yayo yadakamba, “Palibe chifupa chake ata chimojhi icho sichithyoledwe.” 37Ndiipo maleombo ina yakambanjho, “Sampenye uyo adamlasa ni msongha.”
Yesu wazikidwa
Matayo 27:57-61; Maluko 15:42-47; Luka 23:50-56
38Pambuyo pa yameneyo Yusufu wa ku Alimataya, uyo wadali oyaluzidwa wa Yesu, nambho kojhibisa, ndande yakwaopa achogholeli wa Ayahudi. Chimwecho wadampembha Pilato luhusa yotenga thupi la Yesu. Ndiipo wadapita kulichocha. 39Nikodemo uyo wadamchata Yesu ndhawi ya usiku, wadajha ni msingizikano wa manemane ni udi okwanila kilo selasini. 40Ndiipo adalitenga thupi la Yesu, adamanga sanda pamojhi ni manukato, ngati umo chili chikhalidwe cha Ayahudi po zika. 41Pamalo yapo wadapachikidwa Yesu idalipo busitani, pamalo pamenepo chidalipo chiliza icho siwaikidwepo mundhu. 42Nambho ndande ya njhito za Ayahudi zo andaa Siku lo Pumulila, ni ndande chiliza imeneyo idali pafupi, adamzika Yesu mmwemo.

Currently Selected:

Yohana 19: NTNYBL2025

Highlight

Share

Copy

None

Want to have your highlights saved across all your devices? Sign up or sign in