YouVersion Logo
Search Icon

Mt. 4:1-2

Mt. 4:1-2 BLY-DC

Zitatha izi, Mzimu Woyera adatsogolera Yesu kupita ku chipululu kuti Satana akamuyese. Pa masiku makumi anai Yesu adasala zakudya usana ndi usiku, ndipo pambuyo pake adamva njala.

Free Reading Plans and Devotionals related to Mt. 4:1-2