YouVersion Logo
Search Icon

Lk. 5:5-6

Lk. 5:5-6 BLY-DC

Simoni adati, “Aphunzitsi, usiku wonsewu takhalira kugwira ntchito, osapha kanthu, koma chifukwa Inuyo mwatero, chabwino ndiponya makoka.” Tsono iwo adaponyadi makoka, napha nsomba zambirimbiri, kotero kuti makokawo ankayamba kung'ambika.

Free Reading Plans and Devotionals related to Lk. 5:5-6