YouVersion Logo
Search Icon

Lk. 24:2-3

Lk. 24:2-3 BLY-DC

Adapeza chimwala chija chili chogubuduza kale kuchoka pakhomo pa manda aja. Adaloŵa m'mandamo koma sadaupeze mtembo wa Ambuye Yesu.

Free Reading Plans and Devotionals related to Lk. 24:2-3