YouVersion Logo
Search Icon

MATEYU 6:9-10

MATEYU 6:9-10 BLPB2014

Chifukwa chake pempherani inu chomwechi: Atate wathu wa Kumwamba, Dzina lanu liyeretsedwe. Ufumu wanu udze. Kufuna kwanu kuchitidwe, monga Kumwamba chomwecho pansi pano.