YouVersion Logo
Search Icon

MACHITIDWE A ATUMWI 21:13

MACHITIDWE A ATUMWI 21:13 BLPB2014

Pamenepo Paulo anayankha, Muchitanji, polira ndi kundiswera mtima? Pakuti ndakonzeka ine si kumangidwa kokha, komatunso kufera ku Yerusalemu chifukwa cha dzina la Ambuye Yesu.

Free Reading Plans and Devotionals related to MACHITIDWE A ATUMWI 21:13