YouVersion Logo
Search Icon

MACHITIDWE A ATUMWI 20:24

MACHITIDWE A ATUMWI 20:24 BLPB2014

Komatu sindiuyesa kanthu moyo wanga, kuti uli wa mtengo wake kwa ine ndekha; kotero kuti ndikatsirize njira yanga, ndi utumiki ndinaulandira kwa Ambuye Yesu, kuchitira umboni Uthenga Wabwino wa chisomo cha Mulungu.