Bible App logo
Search Icon

Yeremiya 33:6-7

Yeremiya 33:6-7 CCL

“ ‘Pambuyo pake mzindawu ndidzawupatsanso moyo ndi kuwuchiritsa; ndidzachiritsa anthu anga ndi kuwapatsa chitetezo ndi mtendere weniweni. Ndidzawakhazikanso Ayuda ndi Aisraeli ku dziko lawo, ndipo ndidzawabwezera monga mmene analili poyamba.

Video for Yeremiya 33:6-7

Free Reading Plans and Devotionals related to Yeremiya 33:6-7