YouVersion Logo
Search Icon

MACHITIDWE 17:31

MACHITIDWE 17:31 BLP-2018

chifukwa anapangira tsiku limene adzaweruza dziko lokhalamo anthu m'chilungamo, ndi munthu amene anamuikiratu; napatsa anthu onse chitsimikizo, pamene anamuukitsa Iye kwa akufa.