Ajhuku wa akulu adakomana ni akulu adavomelezana chindhu, adaapacha alonda wajha ndalama zambili, adaakambila, “Kambani, ‘Oyaluzidwa wake adajha usiku kuba chitanda chake ife yapo tidagona.’ Nghani izi zikamfikila mlamuli, ife sitikambe naye nianyiimwe simlowa mavuto.”
Alonda adalandila ndalama ni adachita ngati mujha adakambilidwa. Mbili iyi idaenela kwa Ayahudi mbakana lelo.