1
Matayo 26:41
Nyanja
NTNYBL2025
Chezelani ni kupembhela kuti msadalowa mu mayeselo. Mtima ufuna kuchita yayo yafunika, nambho thupi lilibe mbhavu.”
Compare
Explore Matayo 26:41
2
Matayo 26:38
Kumeneko wadaakambila, “Nili ni chisoni chachikulu mumtima mwanga icho chikhoza kunipha. Khalani pano ni muchezele pamojhi ni ine.”
Explore Matayo 26:38
3
Matayo 26:39
Wadapita pachogolo pang'ono, wadagwa panjhi chifufumimba ni kupembhela, “Atate wanga, ngati ikhozeka, nichocheleni chikho ichi cha mavuto! Chipano osati ngati umo nifunila ine, nambho ngati umo mufunila imwe.”
Explore Matayo 26:39
4
Matayo 26:28
uwu nde mwazi wanga uwo uchimikiza chipangano, umwazika ndande ya ambili dala machimo yao yalekeleledwe.
Explore Matayo 26:28
5
Matayo 26:26
Yapo amadya Yesu wadatenga bumunda, wadayamika, wadaubandhula, ni kwapacha oyaluzidwa wake nikukamba, “Tengani mudye, ili nithupi langa.”
Explore Matayo 26:26
6
Matayo 26:27
Ndiipo wadatenga chikho, wadayamika Mnungu, ni kwaapacha oyaluzidwa wake niwakamba, “Mwaonjhe mchimwele chikho ichi
Explore Matayo 26:27
7
Matayo 26:40
Ndiipo wadabwela kwa oyaluzidwa wake ni kwaapheza agona, wadamkambila Petulo, “Ikhala bwanji simdakhoze kuchezelela ni ine ata kwa saa imojhipe?
Explore Matayo 26:40
8
Matayo 26:29
Nikukambilani, sinimwanjho divai iyi mbaka siku ilo sinimwe divai yachipano ni anyiimwe mu Ufumu wa Atate wanga.”
Explore Matayo 26:29
9
Matayo 26:75
Ndiipo Petulo wadakumbukila mau yajha wadakamba Yesu, “Tambala wakali osalile, siunikane katatu.” Wadapita kubwalo, wadalila kwa kubuula.
Explore Matayo 26:75
10
Matayo 26:46
Imani tijhipita. Yujha waning'anamuka watokujha.”
Explore Matayo 26:46
11
Matayo 26:52
Ndiipo Yesu wadamkambila, “Bwezela upanga wako mmalo mwake, pakuti waliyonjhe wakupha kwa upanga, siwaphedwe kwa upanga.
Explore Matayo 26:52
Home
Bible
Plans
Videos