1
Matayo 21:22
Nyanja
NTNYBL2025
Mukakulupilila chindhu chilichonjhe simpembhe mmapembhelo, simulandile.”
Compare
Explore Matayo 21:22
2
Matayo 21:21
Yesu wadakambila, “Zene nikukambilani, ngati simukhulupilile popande kukayikila, mkhoza kuchita osati ichipe nachita pamtengo, nambho mkhoza kulikambila pili ili, ‘Zuka ukajhitaye mnyanja,’ siikhale chimwecho.
Explore Matayo 21:21
3
Matayo 21:9
Gulu la wandhu lidachogolela ni lijha limamchata mbuyo lidakweza mvekelo nilikamba, “Watamandidwe Mwana wa Daudi! Wamwawi yujha wakujha kwa jhina la Ambuye! Matamando kwa Mnungu kumwamba!”
Explore Matayo 21:9
4
Matayo 21:13
ni wadaakambila, “Yalembedwa mmalembo yoyela, ‘Nyumba yanga siikhale nyumba ya mapembhelo, nambho anyiimwe mwaichita mbhanga ya olanda!’”
Explore Matayo 21:13
5
Matayo 21:5
“Mkambileni mwali wa Sayuni, ‘Penya, mfumu wako watokujhela! Mpole ni wakwela pamsana pa phunda, mwana wa phunda.’ ”
Explore Matayo 21:5
6
Matayo 21:42
Yesu wadaafunjha, “Bwanji, simudasome mmalembo ya Mnungu, ‘Mwala uwo adaukana omanga chipano wakala mwala wofunika kupunda pa msingi. Chindhu ichi chachoka kwa Ambuye, nalo litidabwicha?’”
Explore Matayo 21:42
7
Matayo 21:43
“Chipano nikukambilani, Ufumu wa Mnungu siulandidwe kwanu ni kwaapacha wandhu wina anyiyawo osati Ayahudi.
Explore Matayo 21:43
Home
Bible
Plans
Videos