1
Matayo 17:20
Nyanja
NTNYBL2025
Yesu wadaayangha, “Ndande ya chikhulupi chanu chochepa. Nikukambilani uzene, ngati mdakakhala ni chikulupi ngati mbeu ya aladali, mdakakhoza kulikambila phili ili, ‘Chokapo upite yapo’ nalo udakapita. Palibe chindhu icho sichilepeleke kwanu.
Compare
Explore Matayo 17:20
2
Matayo 17:5
Petulo yapo wamakamba chimwecho, mtambo wong'azikila udavinikila, ni mvekelo udaveka kuchoka kumtambo, “Uyu nde Mwana wanga uyo nimkonda, nikondwela nayo kupunda, mveleni iye.”
Explore Matayo 17:5
3
Matayo 17:17-18
Yesu wadaayangha, “Imwe mbadwa wopande chikhulupi ni olakwa! Sinikhale ni anyiimwe mbaka liti? Sinikulimbileni mtima mbaka liti? Jhinayoni pano mnyamatayo.” Ndiipo Yesu wadachinyindila chiwanda, nacho chidamchoka mnyamata, ni wadalama pampajha.
Explore Matayo 17:17-18
Home
Bible
Plans
Videos