1
Matayo 16:24
Nyanja
NTNYBL2025
Ndiipo Yesu wadaakambila oyaluzidwa wake, “Mundhu uyo wafuna kunichata, poyamba wafunika wajhikane mwenewake ni kuutenga mtanda wake, wanichate.
Compare
Explore Matayo 16:24
2
Matayo 16:18
Niine nikukambila iwe Petulo, iwe ni mwala waukulu, ni pamwamba pa mwala umenewo, siniumange mpingo wanga, ni mbhavu za kumdima sizikhoza kulimbana nawo.
Explore Matayo 16:18
3
Matayo 16:19
Nikupacha ufunguo wa ufumu wa kumwamba ni chilichonjhe icho siuchimange pajhiko, sichimangidwe kumwamba, chilichonjhe icho siuchimasule pajhiko, sichimasulidwenjho kumwamba.”
Explore Matayo 16:19
4
Matayo 16:25
Pakuti, mundhu uyo wafuna kuulamicha umoyo wake, siwautaize, ni mundhu uyo siwautaize umoyo wake ndande ya ine, siwaupate.
Explore Matayo 16:25
5
Matayo 16:26
Pakuti, mundhu siwapate phindu lanji wakayapata yonjhe yali pajhiko, nambho wautaize umoyo wake? Kapina mundhu siwachoche chiyani kuti waupate umoyo wake?
Explore Matayo 16:26
6
Matayo 16:15-16
Yesu wadaafunjha, “Bwanji, ni anyiimwe mkamba kuti ine ni yani?” Simoni uyo watanidwa Petulo wadayangha, “Iwe nde Kilisito muomboli, Mwana wa Mnungu wali wamoyo.”
Explore Matayo 16:15-16
7
Matayo 16:17
Yesu wadayangha, “Wapachidwa mwawi iwe Simoni mwana wa Yona, pakuti ichi wachikamba siudavunukulilidwe ni mundhu, nambho Atate wanga a kumwamba.
Explore Matayo 16:17
Home
Bible
Plans
Videos