1
Matayo 10:16
Nyanja
NTNYBL2025
“Vechelani, ine nikutumani anyiimwe ngati mbelele pakati pa mibinji. Mkhale ochenjela ngati njoka, ni apole ngati nghunda.
Compare
Explore Matayo 10:16
2
Matayo 10:39
Mundhu waliyonjhe uyo siwaulonde umoyo wake siwausoweze, nambho waliyonjhe uyo wausoweza umoyo wake ndande ya ine, siwaupate umoyo wa muyaya.”
Explore Matayo 10:39
3
Matayo 10:28
Msadaopa yawo akhoza kukuphani anyiimwe, nambho sakhoza kuyomwecha mizimu yanu. Nambho muopeni yujha wakhoza kuyomwecha thupi pamojhi ni mzimu mumoto wa muyaya.
Explore Matayo 10:28
4
Matayo 10:38
Mundhu uyo siwavomela kuvutika ni kunichata ine, mmeneyo siwakhoza kukhala oyaluzidwa wanga.
Explore Matayo 10:38
5
Matayo 10:32-33
“Mundhu waliyonjhe uyo siwavomele pachogolo pa wandhu kuti iye ni wanga, ine nane sinimvomele pamaso pa Atate wanga yawo ali ku mwamba. Nambho mundhu waliyonjhe uyo siwanikane pachogolo pa wandhu, ine nane sinimkane pamaso pa Atate wanga aku mwamba.”
Explore Matayo 10:32-33
6
Matayo 10:8
Mwaalamiche odwala, ahyucheni akufa, alamicheni a makate, chochani viwanda. Anyiimwe mwapachidwa chajhe, chochani chajhe.
Explore Matayo 10:8
7
Matayo 10:31
Chimwecho msadaopa, anyiimwe amate kupunda kupitilila mbalame!”
Explore Matayo 10:31
8
Matayo 10:34
“Msadaganiza kuti najha kwaachita wandhu akhale kwa mtendele pajhiko. Notho. Sinidajhe kwaachita wandhu akhale kwa mtendele, nambho najha kupeleka upanga.
Explore Matayo 10:34
Home
Bible
Plans
Videos