1
1 AKORINTO 15:58
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
BLPB2014
Chifukwa chake, abale anga okondedwa, khalani okhazikika, osasunthika, akuchuluka mu ntchito ya Ambuye, nthawi zonse, podziwa kuti kuchititsa kwanu sikuli chabe mwa Ambuye.
Compare
Explore 1 AKORINTO 15:58
2
1 AKORINTO 15:57
koma ayamikike Mulungu, amene atipatsa ife chigonjetso mwa Ambuye wathu Yesu Khristu.
Explore 1 AKORINTO 15:57
3
1 AKORINTO 15:33
Musanyengedwe; mayanjano oipa aipsa makhalidwe okoma.
Explore 1 AKORINTO 15:33
4
1 AKORINTO 15:10
Koma ndi chisomo cha Mulungu ndili ine amene ndili; ndipo chisomo chake cha kwa ine sichinakhala chopanda pake, koma ndinagwirira ntchito yochuluka ya iwo onse; koma si ine, koma chisomo cha Mulungu chakukhala ndi ine.
Explore 1 AKORINTO 15:10
5
1 AKORINTO 15:55-56
Imfawe, chigonjetso chako chili kuti? Imfawe, mbola yako ili kuti? Koma mbola ya imfa ndiyo uchimo; koma mphamvu ya uchimo ndiyo chilamulo
Explore 1 AKORINTO 15:55-56
6
1 AKORINTO 15:51-52
Taonani, ndikuuzani chinsinsi; sitidzagona tonse, koma tonse tidzasandulika, m'kamphindi, m'kuthwanima kwa diso, pa lipenga lotsiriza; pakuti lipenga lidzalira, ndipo akufa adzaukitsidwa osavunda, ndipo ife tidzasandulika.
Explore 1 AKORINTO 15:51-52
7
1 AKORINTO 15:21-22
Pakuti monga imfa inadza mwa munthu, kuuka kwa akufa kunadzanso mwa munthu. Pakuti monga mwa Adamu onse amwalira, choteronso mwa Khristu onse akhalitsidwa ndi moyo.
Explore 1 AKORINTO 15:21-22
8
1 AKORINTO 15:53
Pakuti chovunda ichi chiyenera kuvala chisavundi, ndi chaimfa ichi kuvala chosafa.
Explore 1 AKORINTO 15:53
9
1 AKORINTO 15:25-26
Pakuti ayenera kuchita ufumu kufikira ataika adani onse pansi pa mapazi ake. Mdani wotsiriza amene adzathedwa ndiye imfa.
Explore 1 AKORINTO 15:25-26
Home
Bible
Plans
Videos