1
Mateyu 16:24
Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
CCL
Pamenepo Yesu anati kwa ophunzira ake, “Ngati wina aliyense abwera pambuyo panga ayenera kudzikana ndi kutenga mtanda wake ndi kunditsata Ine.
Compare
Explore Mateyu 16:24
2
Mateyu 16:18
Ndipo Ine ndikuwuza iwe kuti ndiwe Petro ndipo pa thanthwe ili Ine ndidzamangapo mpingo wanga ndipo makomo a ku gehena sadzawugonjetsa.
Explore Mateyu 16:18
3
Mateyu 16:19
Ine ndidzakupatsa makiyi a Ufumu wakumwamba, ndipo chilichonse chimene iwe udzachimanga pansi pano chidzamangidwanso kumwamba.”
Explore Mateyu 16:19
4
Mateyu 16:25
Pakuti aliyense amene afuna kupulumutsa moyo wake adzawutaya koma aliyense amene ataya moyo wake chifukwa cha Ine adzawupeza.
Explore Mateyu 16:25
5
Mateyu 16:26
Kodi munthu adzapindula chiyani ngati atapeza zonse za dziko lapansi nataya moyo wake? Kapena munthu angapereke chiyani chosinthana ndi moyo wake?
Explore Mateyu 16:26
6
Mateyu 16:15-16
Iye anafunsa kuti, “Nanga inuyo mumati ndine yani?” Simoni Petro anayankha kuti, “Inu ndinu Khristu, Mwana wa Mulungu wamoyo.”
Explore Mateyu 16:15-16
7
Mateyu 16:17
Yesu anati kwa iye, “Ndiwe wodala Simoni mwana wa Yona, popeza si munthu amene anakuwululira izi koma Atate anga akumwamba.
Explore Mateyu 16:17