1
Levitiko 20:13
Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
CCL
“ ‘Ngati munthu agonana ndi mwamuna mnzake ngati akugonana ndi mkazi, ndiye kuti onsewo achita chinthu cha manyazi. Choncho aphedwe. Magazi awo adzakhala pa mitu pawo.
Compare
Explore Levitiko 20:13
2
Levitiko 20:7
“ ‘Chifukwa chake dzipatuleni ndi kukhala woyera popeza Ine ndine Yehova Mulungu wanu.
Explore Levitiko 20:7
3
Levitiko 20:26
Muzikhala woyera pamaso panga chifukwa Ine Yehova, ndine woyera ndipo ndakupatulani pakati pa anthu a mitundu yonse kuti mukhale anthu anga.
Explore Levitiko 20:26
4
Levitiko 20:8
Ndipo sungani malangizo anga ndi kuwatsata. Ine ndine Yehova amene ndimakuyeretsani.
Explore Levitiko 20:8