1
Levitiko 18:22
Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
CCL
“ ‘Usagonane ndi mwamuna ngati mkazi; chimenecho ndi chinthu chonyansa.
Compare
Explore Levitiko 18:22
2
Levitiko 18:23
“ ‘Usagonane ndi nyama ndi kudziyipitsa nayo. Mkazi asadzipereke kwa nyama kuti agonane nayo. Chimenecho ndi chisokonezo.
Explore Levitiko 18:23
3
Levitiko 18:21
“ ‘Usapereke mwana wako aliyense kuti akhale nsembe yamoto kwa Moleki ndi kuyipitsa dzina la Yehova. Ine ndine Yehova.
Explore Levitiko 18:21