1
Yesaya 8:13
Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
CCL
Yehova Wamphamvuzonse ndiye amene uyenera kumuona kuti ndi woyera, ndiye amene uyenera kumuopa, ndiye amene uyenera kuchita naye mantha
Compare
Explore Yesaya 8:13
2
Yesaya 8:12
“Usamanene kuti ndi chiwembu, chilichonse chimene anthuwa amati ndi chiwembu usamaope zimene anthuwa amaziopa, ndipo usamachite nazo mantha.
Explore Yesaya 8:12
3
Yesaya 8:20
kuti akalandireko mawu enieni ndi malangizo? Ngati anthuwo sayankhula monga mwa mawu awa, mwa iwo mulibe kuwala.
Explore Yesaya 8:20