1
Yesaya 10:27
Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
CCL
Tsiku limenelo katundu wawo adzachotsedwa pa mapewa anu, goli lawo lidzachoka mʼkhosi mwanu; golilo lidzathyoka chifukwa cha kunenepa kwambiri.
Compare
Explore Yesaya 10:27
2
Yesaya 10:1
Tsoka kwa anthu amene amapanga malamulo opanda chilungamo, kwa iwo amene amalemba zongovutitsa anzawo
Explore Yesaya 10:1