1
Eksodo 22:22-23
Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
CCL
“Musazunze mkazi wamasiye kapena mwana wamasiye. Ngati muwazunza ndipo iwo nʼkulirira kwa Ine, ndidzamva kulira kwawo.
Compare
Explore Eksodo 22:22-23
2
Eksodo 22:21
“Musazunze mlendo kapena kumuchitira nkhanza, pakuti inu munali alendo mʼdziko la Igupto.
Explore Eksodo 22:21
3
Eksodo 22:18
“Musayilole mfiti yayikazi kuti ikhale ndi moyo.
Explore Eksodo 22:18
4
Eksodo 22:25
“Ngati mukongoza ndalama kwa mʼbale wanu amene ndi mʼmphawi pakati panu, musadzamuchite monga zimene amachita wokongoza ndalama. Musadzamuyikire chiwongoladzanja.
Explore Eksodo 22:25