1
MATEYU 25:40
Buku Lopatulika
BLP-2018
Ndipo Mfumuyo idzayankha nidzati kwa iwo, Indetu ndinena kwa inu, Chifukwa munachitira ichi mmodzi wa abale anga, ngakhale ang'onong'ono awa, munandichitira ichi Ine.
Compare
Explore MATEYU 25:40
2
MATEYU 25:21
Mbuye wake anati kwa iye, Chabwino, kapolo iwe wabwino ndi wokhulupirika; unali wokhulupirika pa zinthu zazing'ono, ndidzakhazika iwe pa zinthu zambiri; lowa iwe m'chikondwerero cha mbuye wako.
Explore MATEYU 25:21
3
MATEYU 25:29
Pakuti kwa yense amene ali nazo, kudzapatsidwa, ndipo iye adzakhala nazo zochuluka: koma kwa iye amene alibe, kudzachotsedwa, chingakhale chimene anali nacho.
Explore MATEYU 25:29
4
MATEYU 25:13
Chifukwa chake dikirani, pakuti simudziwa tsiku lake, kapena nthawi yake.
Explore MATEYU 25:13
5
MATEYU 25:35
pakuti ndinali ndi njala, ndipo munandipatsa Ine kudya; ndinali ndi ludzu, ndipo munandimwetsa Ine; ndinali mlendo, ndipo munachereza Ine
Explore MATEYU 25:35
6
MATEYU 25:23
Explore MATEYU 25:23
7
MATEYU 25:36
wamaliseche Ine, ndipo munandiveka; ndinadwala, ndipo munadza kucheza ndi Ine; ndinali m'nyumba yandende, ndipo munadza kwa Ine.
Explore MATEYU 25:36
Home
Bible
Plans
Videos