Pakuti yonjhe yayo yadalembedwa mmalembo ya Mnungu, yadalembedwa ndande ya kutiyaluza ife, malembo yameneyo yatithangatila kulimba mtima mumavuto yathu ni kutitondeza, tikhoze kukhala ni chikhulupi.
Alom 15:4
Home
Bible
Plans
Videos