1
Matayo 25:40
Nyanja
NTNYBL2025
Mfumu siwaayanghe, ‘Zene nikukambilani, umo mwamchitila mmojhi wa anyiyawa abale wanga yawo sajhikoza, mwanichitila ine!’”
Linganisha
Chunguza Matayo 25:40
2
Matayo 25:21
Mkulu wake wadamkambila, ‘Wachita bwino, iwe ni mbowa wabwino ni ukhulupilika. Pakuti udakhulupilika kwa vindhu vochepa, chipano sinikupache vindhu va vikulu, majha ukondwele pamojhi ni mkulu wako!’
Chunguza Matayo 25:21
3
Matayo 25:29
Pakuti kila uyo wachitila njhito icho nampacha sinimchuluchile vina nayo siwakhale navo vambili. Nambho mundhu waliyonjhe uyo siwachitila njhito icho nimpacha, ata chaching'ono walinacho siwalandidwe.
Chunguza Matayo 25:29
4
Matayo 25:13
Ndiipo Yesu wadamalizila kukamba, “Mjhipenyelele pakuti simujhiwa siku kapina saa.”
Chunguza Matayo 25:13
5
Matayo 25:35
Nidali ni njala mdanipacha chakudya, ni nidali nilujho mdanipacha majhi ya kumwa, ni nidali mlendo mdanilandila mnyumba zanu.
Chunguza Matayo 25:35
6
Matayo 25:23
Mkulu wake wadakamba, ‘Wachita bwino, iwe ni mbowa wabwino ni okhulupilika. Pakuti udali wokhulupilika kwa vindhu vochepa, sinikuike uimilile vindhu va vikulu, majha ukondwele pamojhi ni mkulu wako!’
Chunguza Matayo 25:23
7
Matayo 25:36
Nidalibe njhalu mdaniveka, nidali odwala mdanidwaza ni nidali mndende mdaniyendela.’
Chunguza Matayo 25:36
Nyumbani
Biblia
Mipango
Video