1
MATEYU 8:26
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
BLPB2014
Ndipo ananena Iye kwa iwo, Muli amantha bwanji, okhulupirira pang'ono inu? Pomwepo Iye anauka, nadzudzula mphepo ndi nyanja, ndipo panagwa bata lalikulu.
Linganisha
Chunguza MATEYU 8:26
2
MATEYU 8:8
Koma kenturiyoyo anavomera nati, Ambuye, sindiyenera kuti mukalowe pansi pa chindwi langa iai; koma mungonena mau, ndipo adzachiritsidwa mnyamata wanga.
Chunguza MATEYU 8:8
3
MATEYU 8:10
Ndipo pakumva ichi, Yesu anazizwa, nati kwa iwo akumtsata, Indetu ndinena kwa inu, ngakhale mwa Israele, sindinapeza chikhulupiriro chotere.
Chunguza MATEYU 8:10
4
MATEYU 8:13
Ndipo Yesu anati kwa kenturiyoyo, Pita, kukhale kwa iwe monga unakhulupirira. Ndipo anachiritsidwa mnyamatayo nthawi yomweyo.
Chunguza MATEYU 8:13
5
MATEYU 8:27
Ndipo anazizwa anthuwo nanena, Ndiye munthu wotani uyu, pakuti ngakhale mphepo ndi nyanja zimvera Iye?
Chunguza MATEYU 8:27
Nyumbani
Biblia
Mipango
Video