1
2 AKORINTO 10:5
Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014
BLPB2014
ndi kugwetsa matsutsano, ndi chokwezeka chonse chimene chidzikweza pokana chidziwitso cha Mulungu, ndi kugonjetsa ganizo lonse kukumvera kwa Khristu
Linganisha
Chunguza 2 AKORINTO 10:5
2
2 AKORINTO 10:4
(pakuti zida za nkhondo yathu sizili za thupi, koma zamphamvu mwa Mulungu zakupasula malinga)
Chunguza 2 AKORINTO 10:4
3
2 AKORINTO 10:3
Pakuti pakuyendayenda m'thupi, sitichita nkhondo monga mwa thupi
Chunguza 2 AKORINTO 10:3
4
2 AKORINTO 10:18
pakuti si iye amene adzitama yekha, koma iye amene Ambuye amtama ali wovomerezeka.
Chunguza 2 AKORINTO 10:18
Nyumbani
Biblia
Mipango
Video