Matayo 27:22-23
Matayo 27:22-23 NTNYBL2025
Pilato wadafunjha, “Nimchite chiyani uyu Yesu watanidwa Kilisito?” Onjhe adakamba “Wapachikidwe pamtanda!” Pilato wadaafunjha, “Ndande yanji? Wachita chindhu chanji choipa?” Adamkambila “Mpachikeni pamtanda!”