YouVersion Logo
Search Icon

Matayo 18

18
Yani waliwamkulu pa Ufumu wa Mnungu
Maluko 9:33-37; Luka 9:46-48
1Ndhawi imeneyo oyaluzidwa adamchata Yesu, adaamfunjha, “Yani uyo wali wamkulu kupitilila wonjhe mu Ufumu wa kumwamba?”
2Yesu wadamtana mwana wamng'ono ni kumwimika pakati pao, 3Ndiipo wadaakambila, “Zene nikukambilani, ngati simng'anamuka ni kulingana ni wana waang'onoang'ono, simulowa mu Ufumu wa kumwamba. 4Waliyonjhe uyo wajhichepecha ngati mwana uyu, nde uyo siwakhale wamkulu mu Ufumu wa kumwamba. 5Uyo wamlandila mwana wamng'ono ngati uyu kwa jhina langa, wanilandila ine.”
Vindhu ivo vimchiticha mundhu wachite machimo
Maluko 9:42-48; Luka 17:1-2
6“Ngati mundhu waliyonjhe uyo wamchiticha mmojhi wa wana yawa kuchita chimo, idakakhala mbasa kwa mundhu mmeneyo wamangidwe mbhelo mkhosi mwake ni kubizidwa kuchilundu. 7Nambho sialage wandhu ajhiko lapanjhi yawo waachiticha yawo amkhulupilila Kilisito kuchita machimo. Vindhu ivo vaachiticha wandhu kuchita machimo lazima vijhe, nambho siwalage mundhu yujha waachiticha wandhu wina kuchita machimo.”
8“Ngati jhanja kapina mwendo wako vikakuchiticha chimo, udule ni kuutaya kutali ni iwe. Mbasa ulowe mu umoyo wamuyaya popande jhanja kapina mwendo, kusiyana ni kutaidwa pamoto uwo siuthima wa muyaya uli ni manja yawili ni miendo yako iwili. 9Diso lako nalo ngati likuchiticha kuchita uchimo, lizule ni ulitae patali. Mbasa ukalowe mu umoyo wosatha muyaya uli ni diso limojhi, kusiyana kutaidwa pamoto wosatha wa muyaya uli ni maso yonjhe yawili.”
Chifani cha mbelele iyo yasowa
Luka 15:3-7
10“Khalani maso! Musamdamdelela mmojhi wa wang'ono yawa, pakuti nikukambilani, atumiki wao a kumwamba siku zonjhe ali pamojhi ni Mnungu. 11Pakuti Mwana wa Mundhu wadajha kwaombola anyiwajha ali ngati asowa.”
12“Muona bwanji ngati mundhu wali ni mbelele miya mojha, ikasowa imojhi, wachita bwanji? Wazisia zijha tisini ni tisa mkhola, nikupita kuifunafuna ijha yasowa. 13Uzene nikukambilani, wakaipeza, siwakondwe kupunda ndande ya mbelele imojhi kusiyana ni zijha tisiini ni tisa izo sizidasowe. 14Chinchijha, Atate wanu a kumwamba siafuna ata mmojhi wa anyiyawa wang'ono wasowe.”
Mbale wako yapo wachita machimo
15“Ngati mbale wako wakalakwila, mchate umkambile kulakwa kwake muli awilipe. Wakakuvela siikhale wampata mbale wako. 16Nambho ngati siwakane kukuvela, funa mundhu mwina mmojhi kapina awili pamojhi ni iwe, kuti mau lililonjhe lichimikizike kwa amboni awili kapina atatu ili mavuto yathele, ngati umo yalembedwa mmalembo. 17Ngati siwakane kwaavela achamenewo, ukambile mpingo, ngati siwakane kuuvela mpingo, basi mchite mundhu mmeneyo ngati mundhu uyo siwamjhiwa Mungu kapima wolandila nsongho.”
Kukaniza ni kuloleza
18“Zene ikukambilani, yayo simuyamange pajhiko la panjhi chinchijha siyamangidwe kumwamba, ni icho simuchimasule pajhiko la panjhi chinchijha sichimasulidwe kumwamba.
19“Zene nikukambilani, awili pakati panu akavomelezana pajhiko la panjhi kuusu chilichonjhe icho afuna kupembha, Atate wanga a kumwamba siakuchitileni. 20Pakuti yapo asonghana wandhu awili kapina atatu kwa jhina langa, ine nili pamojhi nao.”
Chifani cha mbowa uyo siwalekelela
21Ndiipo Petulo wadamchata Yesu ni kumfunjha, “Ambuye, mbale wanga wakanililakwila, nimlekelele kangati? Bwanji, mala saba ikwana?”
22Yesu wadamuyangha, “Sinikamba mala sabape, nambho saba mala sabini. 23Ufumu wa kumwamba uli chimwechi, mfumu mmojhi wamafuma kuchita chiwelengelo cha chuma chake iye pamojhi ni mbowa zake. 24Yapo wadayamba kuwelengecha, mundhu mmojhi uyo wadakongola ndalama miliyoni zambili, wadapelekedwa kwaiye. 25Pakuti wadalibe chindhu chobweza ngongole, mfumu wake wadalamula kuti iye ni mkazake ni wana wake ni vonjhe ivo wadalinavo vigulichidwe, kuti ibwezedwe ngongole. 26Mbowa yujha wadamgwadila ni kukamba, ‘Unilengele lisungu, sinibweze ngongole yako yonjhe.’ 27Mkuluyo wadamlengela lisungu, wadamlekelela ngongole yake ni kumsiya wajhipita.”
28“Nambho mbowa yujha yapo wamatuluka kubwalo wadakomana ni mbowa mnjake uyo wadamkongola ndalama zokwana laki imojhi. Wadamgwila ni kumkhaba pakhosi, niwakamba, ‘Bweza ndalama zanga!’ 29Mbowa mnjake yujha wadamgwadila ni kumpembha, ‘Nilengele lisungu, sinikubwezele ndalama yako yonjhe.’ 30Nambho iye wadakana. Wadampeleka kundende mbaka yapo siwabweze ndalamazo. 31Mbowa wina yapo adaona yayo yadachitika, adadandaula kupunda, nawo adapita kumkambila mfumu wao kila chindhu icho yadachokela. 32Ndiipo yujha mfumu wadamtana mnyumba yujha mbowa, wadamkambila, ‘Iwe mbowa woipa! Ine nidakulekelela ngongole zako zonjhe ndande udanipembha, ni nidachita chimwecho. 33Bwanji, iwe siudafunike kumlengela lisungu mnjako, ngati umo nakulengela ine?’ 34Chimwecho mfumu wake yujha wadakwiya kupunda, wadampeleka kundende mbowa wake yujha kuti wavutike mbaka yapo siwabweze ngongole yonjhe.”
35Yesu wadamaliza pokamba, “Umu ndeumo Atate wanga akumwamba siakuchiteni ngati simwaalekelela achanjanu volakwa vao.”

Currently Selected:

Matayo 18: NTNYBL2025

Highlight

Share

Copy

None

Want to have your highlights saved across all your devices? Sign up or sign in