YouVersion Logo
Search Icon

Luka 19:5-6

Luka 19:5-6 NTNYBL2025

Yesu yapo wadafika pamalo yameneyo, wadapenya mmwamba mwa mtengo ni kumkambila, “Zakayo, chika chisanga, pakuti lelo sinikhale mlendo kukhomo lako.” Zakayo wadachika chisanga ni kumlandila Yesu kwa kukondwela.