YouVersion Logo
Search Icon

Mk. 10:6-8

Mk. 10:6-8 BLY-DC

Komatu pachiyambi paja, pamene Mulungu adalenga zonse, adaŵalenga anthu, wina wamwamuna wina wamkazi. Nchifukwa chake mwamuna azisiya atate ndi amai, nakaphatikizana ndi mkazi wake, ndipo aŵiriwo adzasanduka thupi limodzi. Choncho tsopano salinso aŵiri, koma thupi limodzi.

Free Reading Plans and Devotionals related to Mk. 10:6-8