YouVersion Logo
Search Icon

Mt. 24:7-8

Mt. 24:7-8 BLY-DC

Mitundu yosiyanasiyana idzaukirana, maiko osiyanasiyana adzamenyana nkhondo. Kudzakhala njala, ndipo kudzachita zivomezi ku malo osiyanasiyana. Tsono zonsezitu nkuyamba chabe kwa mavuto.

Free Reading Plans and Devotionals related to Mt. 24:7-8