Mt. 14:16-17
Mt. 14:16-17 BLY-DC
Koma Yesu adaŵauza kuti, “Palibe chifukwa choti achokere. Inuyo apatseni chakudya.” Iwo adati, “Pano tili ndi buledi msanu yekha ndi nsomba ziŵiri, basi.”