YouVersion Logo
Search Icon

Lk. 7:47-48

Lk. 7:47-48 BLY-DC

Mwakuti kunena zoona, chikondi chachikulu chimene iyeyu waonetsa, chikutsimikiza kuti Mulungu wamkhululukiradi machimo ake amene ali ochuluka. Koma munthu amene wakhululukidwa zochepa, amangokonda pang'ono.” Ndipo Yesu adauza mai uja kuti, “Machimo ako akhululukidwa.”

Verse Image for Lk. 7:47-48

Lk. 7:47-48 - Mwakuti kunena zoona, chikondi chachikulu chimene iyeyu waonetsa, chikutsimikiza kuti Mulungu wamkhululukiradi machimo ake amene ali ochuluka. Koma munthu amene wakhululukidwa zochepa, amangokonda pang'ono.”
Ndipo Yesu adauza mai uja kuti, “Machimo ako akhululukidwa.”

Free Reading Plans and Devotionals related to Lk. 7:47-48