YouVersion Logo
Search Icon

AROMA 1:20

AROMA 1:20 BLPB2014

Pakuti chilengedwere dziko lapansi zaoneka bwino zosaoneka zake ndizo mphamvu yake yosatha ndi umulungu wake; popeza zazindikirika ndi zinthu zolengedwa, kuti iwo adzakhale opanda mau akuwiringula

Video for AROMA 1:20