YouVersion Logo
Search Icon

AFILIPI 2:14-15

AFILIPI 2:14-15 BLPB2014

Chitani zonse kopanda madandaulo ndi makani, kuti mukakhale osalakwa ndi oona, ana a Mulungu opanda chilema pakati pa mbadwo wokhotakhota ndi wopotoka, mwa iwo amene muonekera monga mauniko m'dziko lapansi