YouVersion Logo
Search Icon

MATEYU 6:3-4

MATEYU 6:3-4 BLPB2014

Koma iwe popatsa mphatso zachifundo, dzanja lako lamanzere lisadziwe chimene lichita dzanja lako lamanja; kotero kuti mphatso zako zachifundo zikhale zam'tseri; ndipo Atate wako wakuona m'tseri adzakubwezera iwe.

Free Reading Plans and Devotionals related to MATEYU 6:3-4