YouVersion Logo
Search Icon

OWERUZA 6:11

OWERUZA 6:11 BLPB2014

Pamenepo anadza mthenga wa Yehova, nakhala patsinde pa thundu wokhala m'Ofura, wa Yowasi Mwabiyezere; ndi mwana wake Gideoni analikuomba tirigu m'mopondera mphesa, awabisire Amidiyani.

Video for OWERUZA 6:11

Free Reading Plans and Devotionals related to OWERUZA 6:11