YouVersion Logo
Search Icon

GENESIS 49:8-9

GENESIS 49:8-9 BLPB2014

Yuda, abale ako adzakuyamika iwe; dzanja lako lidzakhala pa khosi la adani ako; ana amuna a atate wako adzakuweramira. Yuda ndi mwana wa mkango, kuchokera kuzomotola, mwananga, wakwera; anawerama pansi, anabwatama ngati mkango, ndipo ngati mkango waukazi; ndani adzamukitsa iye?