YouVersion Logo
Search Icon

EKSODO 32:5-6

EKSODO 32:5-6 BLPB2014

Pakuchiona Aroni, anamanga guwa la nsembe patsogolo pake; ndipo Aroni anafuula nati, Mawa aliko madyerero a Yehova. Ndipo m'mawa mwake anauka mamawa, nafukiza nsembe zopsereza, nabwera nazo nsembe zamtendere; ndi anthu anakhala pansi kudya ndi kumwa, nauka kusewera.

Free Reading Plans and Devotionals related to EKSODO 32:5-6