EKSODO 29:45-46
EKSODO 29:45-46 BLPB2014
Ndipo ndidzakhala pakati pa ana a Israele, ndi kukhala Mulungu wao. Ndipo adzadziwa kuti Ine ndine Yehova Mulungu wao, amene ndinawatulutsa m'dziko la Ejipito, kuti ndikhale pakati pao. Ine ndine Yehova Mulungu wao.