YouVersion Logo
Search Icon

EKSODO 22:22-23

EKSODO 22:22-23 BLPB2014

Musazunza mkazi wamasiye, kapena mwana wamasiye aliyense. Ukawazunza ndi kakuti konse, nakandilirira pang'ono ponse iwowa, ndidzamvadi kulira kwao

Free Reading Plans and Devotionals related to EKSODO 22:22-23